Tsatsi

  • 9 years ago
Tsatsi ndi makhwala abwino kwambili amathandiza pa mene muthu wapsa ndi moto makhwalawa ndi abwino chifukwa ngati muthu wapsa nkupaka tsatsi pa bala pake pamagwirana mwa nsanga ndipo sipachedwa kupola ngati mwa vulala yesani kugwiritsa tchito makhwala atsatsi ndipo mudzasangalala nawo.